Yohane 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu nʼkuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ mogwirizana ndi mwambo umene Ayuda ankatsatira poika maliro. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:40 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 20
40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu nʼkuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ mogwirizana ndi mwambo umene Ayuda ankatsatira poika maliro.