Yohane 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Popeza linali Tsiku Lokonzekera+ Chikondwerero cha Ayuda, ndipo mandawo anali pafupi, iwo anaika Yesu mmenemo.
42 Popeza linali Tsiku Lokonzekera+ Chikondwerero cha Ayuda, ndipo mandawo anali pafupi, iwo anaika Yesu mmenemo.