Yohane 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya wa ku Magadala anapita kumandako* mʼmawa kwambiri,+ kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamandawo.*+
20 Tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya wa ku Magadala anapita kumandako* mʼmawa kwambiri,+ kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamandawo.*+