Yohane 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Simoni Petulo anati: “Ine ndikupita kukapha nsomba.” Enawonso anati: “Ifenso tipita nawe.” Iwo anapitadi nʼkukwera ngalawa, koma mkati mwa usiku umenewo sanaphe kanthu.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:3 Tsanzirani, ptsa. 202-203 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, tsa. 2511/1/1988, tsa. 31
3 Ndiyeno Simoni Petulo anati: “Ine ndikupita kukapha nsomba.” Enawonso anati: “Ifenso tipita nawe.” Iwo anapitadi nʼkukwera ngalawa, koma mkati mwa usiku umenewo sanaphe kanthu.+