Yohane 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Ponyani ukonde kumbali yakudzanja lamanja kwa ngalawayo ndipo mupeza kenakake.” Choncho anaponyadi ukondewo, koma sanathenso kuukokera mungalawa chifukwa cha kuchuluka kwa nsomba.+
6 Iye anawauza kuti: “Ponyani ukonde kumbali yakudzanja lamanja kwa ngalawayo ndipo mupeza kenakake.” Choncho anaponyadi ukondewo, koma sanathenso kuukokera mungalawa chifukwa cha kuchuluka kwa nsomba.+