Yohane 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, wophunzira amene Yesu ankamukonda kwambiri uja+ anauza Petulo kuti: “Ndi Ambuye!” Simoni Petulo atamva kuti ndi Ambuye, anavala malaya ake akunja, chifukwa anali maliseche,* ndipo analumphira mʼnyanja.
7 Zitatero, wophunzira amene Yesu ankamukonda kwambiri uja+ anauza Petulo kuti: “Ndi Ambuye!” Simoni Petulo atamva kuti ndi Ambuye, anavala malaya ake akunja, chifukwa anali maliseche,* ndipo analumphira mʼnyanja.