-
Yohane 21:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Yesu anawauza kuti: “Bwerani mudzadye chakudya chamʼmawa.” Panalibe ngakhale mmodzi mwa ophunzirawo amene analimba mtima kumufunsa kuti: “Ndinu ndani?” chifukwa ankadziwa kuti ndi Ambuye.
-