-
Yohane 21:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndithudi ndikukuuza iwe, pamene unali mnyamata, unkavala wekha nʼkupita kumene ukufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka ndipo adzakunyamula nʼkupita nawe kumene iwe sukufuna.”
-