Yohane 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Petulo anatembenuka nʼkuona wophunzira amene Yesu ankamukonda uja+ akuwatsatira. Wophunzira ameneyu ndi amene pa chakudya chamadzulo chija anatsamira pachifuwa cha Yesu nʼkumufunsa kuti: “Ambuye, ndi ndani amene akufuna kukuperekani?” Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:20 Nsanja ya Olonda,7/1/2015, tsa. 15
20 Petulo anatembenuka nʼkuona wophunzira amene Yesu ankamukonda uja+ akuwatsatira. Wophunzira ameneyu ndi amene pa chakudya chamadzulo chija anatsamira pachifuwa cha Yesu nʼkumufunsa kuti: “Ambuye, ndi ndani amene akufuna kukuperekani?”