Machitidwe 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa nthawi imene anasonkhana ndi ophunzirawo, anawapatsa malangizo akuti: “Musachoke mu Yerusalemu,+ koma muyembekezere zimene Atate analonjeza,+ zomwe ndinakuuzani.
4 Pa nthawi imene anasonkhana ndi ophunzirawo, anawapatsa malangizo akuti: “Musachoke mu Yerusalemu,+ koma muyembekezere zimene Atate analonjeza,+ zomwe ndinakuuzani.