Machitidwe 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atamaliza kulankhula zimenezi, anatengedwa kupita mumlengalenga iwo akuona, ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 11
9 Atamaliza kulankhula zimenezi, anatengedwa kupita mumlengalenga iwo akuona, ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+