Machitidwe 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anabwerera ku Yerusalemu,+ kuchokera kuphiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.* Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:12 Nsanja ya Olonda,10/1/2008, tsa. 11
12 Kenako anabwerera ku Yerusalemu,+ kuchokera kuphiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*