Machitidwe 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika mumzindawo anapita mʼchipinda chamʼmwamba, mmene ankakhala. Panali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wodzipereka uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 18 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 11
13 Atafika mumzindawo anapita mʼchipinda chamʼmwamba, mmene ankakhala. Panali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wodzipereka uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+