-
Machitidwe 1:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho nʼkofunika kuti alowedwe mʼmalo ndi mmodzi mwa anthu amene ankayenda nafe pa nthawi yonse imene Ambuye Yesu ankachita zinthu zosiyanasiyana pakati pathu.
-