Machitidwe 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 13-146/1/1990, ptsa. 11-12
4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+