Machitidwe 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi. Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndiponso laulemerero la Yehova* lisanafike. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:20 Tsiku la Yehova, tsa. 36 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 13-1412/15/1997, ptsa. 16-17
20 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi. Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndiponso laulemerero la Yehova* lisanafike.