-
Machitidwe 3:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno panali mwamuna wina amene anabadwa ali wolumala. Tsiku lililonse ankamunyamula nʼkumukhazika pafupi ndi khomo la kachisi lotchedwa Geti Lokongola, kuti azipempha mphatso zachifundo kwa anthu olowa mʼkachisimo.
-