Machitidwe 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu uja ankangoyendabe ndi Petulo ndi Yohane osawasiya, ndipo gulu lonse la anthu linathamangira kwa iwo pamalo otchedwa Khonde la Zipilala la Solomo,+ likudabwa kwambiri. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 13
11 Munthu uja ankangoyendabe ndi Petulo ndi Yohane osawasiya, ndipo gulu lonse la anthu linathamangira kwa iwo pamalo otchedwa Khonde la Zipilala la Solomo,+ likudabwa kwambiri.