-
Machitidwe 3:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Petulo ataona zimenezi, anauza anthuwo kuti: “Aisiraeli inu, nʼchifukwa chiyani mukudabwa nazo zimenezi? Nʼchifukwa chiyani mukutiyangʼanitsitsa ngati kuti tamuyendetsa ndi mphamvu zathu kapena chifukwa cha kudzipereka kwathu kwa Mulungu?
-