Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa ndipo ife ndife mboni za nkhani imeneyi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2140
15 Munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa ndipo ife ndife mboni za nkhani imeneyi.+