-
Machitidwe 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho mʼdzina lake komanso chifukwa choti timakhulupirira dzina lakelo, munthu amene mukumuona ndiponso kumudziwayu wachira. Chikhulupiriro chimene ife tili nacho chifukwa cha iye chachititsa kuti achiriretu ngati mmene nonsenu mukuonera.
-