Machitidwe 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo aneneri onse, kuyambira pa Samueli mpaka aneneri onse amene anabwera mʼmbuyo mwake, onse amene analosera, ananena mosapita mʼmbali za masiku amenewa.+
24 Ndipo aneneri onse, kuyambira pa Samueli mpaka aneneri onse amene anabwera mʼmbuyo mwake, onse amene analosera, ananena mosapita mʼmbali za masiku amenewa.+