Machitidwe 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba+ anamutumiza kwa inu, kuti adzakudalitseni pobweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:26 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 13
26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba+ anamutumiza kwa inu, kuti adzakudalitseni pobweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.”