-
Machitidwe 4:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma Petulo ndi Yohane anawayankha kuti: “Weruzani nokha, ngati nʼzoyenera pamaso pa Mulungu kumvera inu mʼmalo momvera Mulunguyo.
-