-
Machitidwe 4:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Atawamasula anapita kwa okhulupirira anzawo, ndipo anawafotokozera zonse zimene ansembe aakulu ndi akulu anawauza.
-