Machitidwe 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zimene zimakhala mmenemo.+
24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zimene zimakhala mmenemo.+