Machitidwe 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pogwiritsa ntchito mzimu woyera, inu munanena kudzera pakamwa pa kholo lathu Davide+ mtumiki wanu kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe ndiponso nʼchifukwa chiyani mitundu ya anthu ikuganizira* zinthu zopanda pake? Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:25 Nsanja ya Olonda,7/15/2004, tsa. 177/1/1990, tsa. 27 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 23-24
25 Pogwiritsa ntchito mzimu woyera, inu munanena kudzera pakamwa pa kholo lathu Davide+ mtumiki wanu kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani anthu a mitundu ina akuchita chipolowe ndiponso nʼchifukwa chiyani mitundu ya anthu ikuganizira* zinthu zopanda pake?