Machitidwe 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipotu panalibe aliyense amene ankasowa kanthu.+ Onse amene anali ndi minda kapena nyumba, ankagulitsa nʼkubweretsa ndalamazo.
34 Ndipotu panalibe aliyense amene ankasowa kanthu.+ Onse amene anali ndi minda kapena nyumba, ankagulitsa nʼkubweretsa ndalamazo.