Machitidwe 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Petulo anati: “Hananiya, nʼchifukwa chiyani Satana wakulimbitsa mtima kuti unamize+ mzimu woyera+ nʼkubisa ndalama zina za mundawo? Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:3 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 14
3 Koma Petulo anati: “Hananiya, nʼchifukwa chiyani Satana wakulimbitsa mtima kuti unamize+ mzimu woyera+ nʼkubisa ndalama zina za mundawo?