Machitidwe 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Petulo anamufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani awirinu munagwirizana kuti muyese mzimu wa Yehova?* Ukudziwa? Anthu amene anapita kukaika mwamuna wako mʼmanda ali pakhomo. Nawenso akunyamula nʼkutuluka nawe.”
9 Kenako Petulo anamufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani awirinu munagwirizana kuti muyese mzimu wa Yehova?* Ukudziwa? Anthu amene anapita kukaika mwamuna wako mʼmanda ali pakhomo. Nawenso akunyamula nʼkutuluka nawe.”