Machitidwe 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthuwo ankabweretsa odwala mʼmisewu nʼkuwagoneka pamabedi angʼonoangʼono ndi pamphasa kuti Petulo akamadutsa, chithunzithunzi chake chokha chifike pa ena mwa odwalawo.+
15 Anthuwo ankabweretsa odwala mʼmisewu nʼkuwagoneka pamabedi angʼonoangʼono ndi pamphasa kuti Petulo akamadutsa, chithunzithunzi chake chokha chifike pa ena mwa odwalawo.+