-
Machitidwe 5:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atamva zimenezi, mʼmawa kwambiri analowa mʼkachisi nʼkuyamba kuphunzitsa.
Koma mkulu wa ansembe ndi onse amene anali naye anasonkhanitsa Khoti Lalikulu la Ayuda ndiponso akulu onse a Aisiraeli. Kenako anatumiza alonda kundende kuja kuti akatenge atumwiwo nʼkubwera nawo.
-