-
Machitidwe 5:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma alonda aja atafika, sanawapeze mʼndendemo. Choncho anabwerera nʼkukanena zimenezi.