-
Machitidwe 5:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Woyangʼanira kachisi ndi ansembe aakulu atamva zimenezi, anathedwa nzeru chifukwa sankadziwa kuti zitha bwanji.
-