Machitidwe 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zitatero woyangʼanira kachisiyo ananyamuka ndi alonda ake nʼkukawatenga. Koma sanawatenge mwachiwawa, poopa kuponyedwa miyala ndi anthu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2020, tsa. 31
26 Zitatero woyangʼanira kachisiyo ananyamuka ndi alonda ake nʼkukawatenga. Koma sanawatenge mwachiwawa, poopa kuponyedwa miyala ndi anthu.+