Machitidwe 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 kuti: “Tinakulamulani mwamphamvu kuti musaphunzitsenso mʼdzina limeneli.+ Koma mwadzaza Yerusalemu yense ndi mfundo zimene mukuphunzitsa ndipo mwatsimikiza mtima kuti ife tikhale ndi mlandu wa magazi a munthu ameneyu.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:28 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 37 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 21
28 kuti: “Tinakulamulani mwamphamvu kuti musaphunzitsenso mʼdzina limeneli.+ Koma mwadzaza Yerusalemu yense ndi mfundo zimene mukuphunzitsa ndipo mwatsimikiza mtima kuti ife tikhale ndi mlandu wa magazi a munthu ameneyu.”+