-
Machitidwe 5:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Kenako kunabwera Yudasi wa ku Galileya mʼmasiku a kalembera. Anthu ambiri anakopeka naye ndipo ankamutsatira. Koma nayenso anafa, ndipo onse amene ankamutsatira anabalalika.
-