-
Machitidwe 5:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Choncho mmene zinthu zilili apapa, ndikukuuzani kuti asiyeni anthu amenewa musalimbane nawo. Chifukwa ngati zolinga zawo kapena ntchito iyi ikuchokera kwa anthu, sipita patali.
-