Machitidwe 5:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo anamvera malangizo akewa ndipo anaitanitsa atumwiwo. Ndiyeno anangowakwapula*+ nʼkuwalamula kuti asiye kulankhula mʼdzina la Yesu, kenako anawamasula.
40 Iwo anamvera malangizo akewa ndipo anaitanitsa atumwiwo. Ndiyeno anangowakwapula*+ nʼkuwalamula kuti asiye kulankhula mʼdzina la Yesu, kenako anawamasula.