Machitidwe 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu onsewo anasangalala ndi mawu amenewa moti anasankha Sitefano, munthu wa chikhulupiriro cholimba ndiponso wodzaza ndi mzimu woyera. Anasankhanso Filipo,+ Purokoro, Nikanora, Timoni, Paremena ndi Nikolao wa ku Antiokeya amene analowa Chiyuda. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2016, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 18
5 Anthu onsewo anasangalala ndi mawu amenewa moti anasankha Sitefano, munthu wa chikhulupiriro cholimba ndiponso wodzaza ndi mzimu woyera. Anasankhanso Filipo,+ Purokoro, Nikanora, Timoni, Paremena ndi Nikolao wa ku Antiokeya amene analowa Chiyuda.