Machitidwe 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira.+ Chiwerengero cha ophunzira chinkawonjezeka kwambiri+ mu Yerusalemu. Ndipo ansembe ambiri anakhala okhulupirira.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:7 Nsanja ya Olonda,4/1/2001, ptsa. 10-11
7 Zitatero mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira.+ Chiwerengero cha ophunzira chinkawonjezeka kwambiri+ mu Yerusalemu. Ndipo ansembe ambiri anakhala okhulupirira.+