-
Machitidwe 6:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kenako ananyengerera amuna ena mwamseri kuti anene kuti: “Tamumva ife ameneyu akulankhula zinthu zonyoza Mose ndi Mulungu.”
-