Machitidwe 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma sanamʼpatsemo cholowa chilichonse, ngakhale kadera kakangʼono. Mʼmalomwake anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli kuti likhale cholowa chake, ndi cha mbadwa* zake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo analibe mwana.
5 Koma sanamʼpatsemo cholowa chilichonse, ngakhale kadera kakangʼono. Mʼmalomwake anamulonjeza kuti adzamupatsa dzikoli kuti likhale cholowa chake, ndi cha mbadwa* zake,+ ngakhale kuti pa nthawiyo analibe mwana.