Machitidwe 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo anamupulumutsa mʼmavuto ake onse. Komanso ankamukonda ndipo ankamuthandiza kuti azichita zinthu mwanzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Faraoyo anapatsa Yosefe udindo woti aziyangʼanira Iguputo ndi nyumba yake yonse.+
10 ndipo anamupulumutsa mʼmavuto ake onse. Komanso ankamukonda ndipo ankamuthandiza kuti azichita zinthu mwanzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Faraoyo anapatsa Yosefe udindo woti aziyangʼanira Iguputo ndi nyumba yake yonse.+