Machitidwe 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ku Iguputo ndi ku Kanani konse kunagwa njala moti kunali mavuto aakulu. Ndipo makolo athuwo sankapeza chakudya.+
11 Kenako ku Iguputo ndi ku Kanani konse kunagwa njala moti kunali mavuto aakulu. Ndipo makolo athuwo sankapeza chakudya.+