Machitidwe 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa ulendo wachiwiri Yosefe anadziulula kwa azichimwene ake, ndipo Farao anadziwa za abale ake a Yosefe ndi makolo ake.+
13 Pa ulendo wachiwiri Yosefe anadziulula kwa azichimwene ake, ndipo Farao anadziwa za abale ake a Yosefe ndi makolo ake.+