Machitidwe 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndiponso abale ake onse.+ Ndipo onse pamodzi analipo anthu 75.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Nsanja ya Olonda,9/15/2002, tsa. 27
14 Choncho Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndiponso abale ake onse.+ Ndipo onse pamodzi analipo anthu 75.+