Machitidwe 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako mafupa awo anawatenga nʼkupita nawo ku Sekemu. Anakawaika mʼmanda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori ku Sekemuko.+
16 Kenako mafupa awo anawatenga nʼkupita nawo ku Sekemu. Anakawaika mʼmanda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori ku Sekemuko.+