Machitidwe 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumu imeneyi inachenjerera anthu a mtundu wathu komanso inakakamiza makolo athuwo kuti azitaya makanda awo nʼcholinga choti asakhale ndi moyo.+
19 Mfumu imeneyi inachenjerera anthu a mtundu wathu komanso inakakamiza makolo athuwo kuti azitaya makanda awo nʼcholinga choti asakhale ndi moyo.+