-
Machitidwe 7:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ataona mmodzi wa abale akewo akuzunzidwa ndi munthu wa ku Iguputo, anamuteteza ndipo anabwezera popha munthu wa ku Iguputoyo.
-